Psalms 4:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikamaitana, mundiyankhe Inu Mulungu, Mtetezi wanga. Mudabwera kudzandithandiza pamene ndinali m'mavuto. Mundichitire chifundo, ndi kumvera pemphero langa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Neginoto. Salimo la Davide. Pakufuula ine mundiyankhe, Mulungu wa chilungamo changa; pondichepera mwandikulitsira malo. Ndichitireni chifundo, imvani pemphero langa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe wa zida za zingwe. Salimo la Davide. Ndiyankheni pamene ndiyitana Inu, Inu Mulungu wa chilungamo changa. Pumulitseni ku zowawa zanga; chitireni chifundo ndi kumva pemphero langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakupfuula ine mundiyankhe, Mulungu wa cilungamo canga; Pondicepera mwandikulitsira malo: Ndicitireni cifundo, imvani pemphero langa.