Psalms 4:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu inu, mudzaleka liti kunyoza ulemu wanga? Bwanji mukukondabe zinthu zachabechabe? Bwanji mukulakalakabe zinthu zonama?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amuna inu, ulemu wanga udzakhala wamanyazi kufikira liti? Mudzakonda zachabe, ndi kufunafuna bodza kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu inu, mpaka liti mudzakhala mukusandutsa ulemerero wanga kukhala manyazi? Mpaka liti mudzakonda zachabe ndi kufuna milungu yabodza? Sela.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amuna inu, ulemu wanga udzakhala wamanyazi kufikira liti? Mudzakonda zacabe, ndi kufunafuna bodza kufikira liti?