Psalms 4:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsono mudziŵe kuti Chauta wadzipatulira Iye yemwe anthu olungama. Chauta amamva ndikamuitana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma dziwani kuti Yehova anadzipatulira yekha womkondayo, adzamva Yehova m'mene ndimfuulira Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziwani kuti Yehova wadziyikira padera anthu okhulupirika; Yehova adzamva pamene ndidzamuyitana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma dziwani kuti Yehova anadzipatulira yekha womkondayo Adzamva Yehova m'mene ndimpfuulira Iye,