Psalms 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alipo ambiri amene amati, “Ndani angatiwonetse zabwino? Mutiyang'ane ndi chikondi chanu, Inu Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambiri amati, Adzationetsa chabwino ndani? Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambiri akufunsa kuti, “Ndani angationetse chabwino chilichonse?” Kuwunika kwa nkhope yanu kutiwalire, Inu Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambiri amati, Adzationetsa cabwino ndani? Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.