Psalms 4:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu mwandisangalatsa mtima kwambiri, kupambana anthu a zakudya ndi zakumwa zambiri!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwapatsa chimwemwe mumtima mwanga, chakuposa chao m'nyengo yakuchuluka dzinthu zao ndi vinyo wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwadzaza mtima wanga ndi chimwemwe chachikulu kuposa kuchuluka kwa tirigu wawo ndi vinyo watsopano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwapatsa cimwemwe mumtima mwanga, Cakuposa cao m'nyengo yakucuruka dzinthu zao ndi vinyo wao.