Psalms 40:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mavuto osaŵerengeka andizinga, machimo anga andigwira, kotero kuti sindingathe kuwona populumukira, ngambiri kupambana tsitsi la kumutu kwanga, ndipo ndataya mtima kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga, zochimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya; ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandichokera mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mavuto osawerengeka andizungulira; machimo anga andigonjetsa, ndipo sindingathe kuona. Alipo ambiri kuposa tsitsi la mʼmutu mwanga, ndipo mtima wanga ukufowoka mʼkati mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga, Zocimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya; Ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandicokera mtima.