Psalms 40:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ofunafuna moyo wanga, muŵachititse manyazi ndi kuŵasokoneza. Okhumba kundipweteka, abwezedwe m'mbuyo ndi kunyozedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Achite manyazi nadodome iwo akulondola moyo wanga kuti auononge. Abwerere m'mbuyo, nachite manyazi iwo okondwera kundichitira choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse amene akufunafuna kuchotsa moyo wanga achititsidwe manyazi ndi kusokonezedwa; onse amene amakhumba chiwonongeko changa abwezedwe mwamanyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Acite manyazi nadodome Iwo akulondola moyo wanga kuti auononge: Abwerere m'mbuyo, nacite manyazi iwo okondwera kundicitira coipa.