Psalms 40:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwodala munthu amene amadalira Chauta, munthu amene sapatukira ku mafano kapena kutsata milungu yonama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi wodala munthu amakhulupirira Yehova; amene sayembekezera kwa odzikuza, kapena kwa amene amatembenukira kwa milungu yabodza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; Wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza.