Psalms 40:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakonda kuchita zimene mumafuna, Inu Mulungu wanga, malamulo anu ali mumtima mwanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuchita chikondwero chanu kundikonda, Mulungu wanga; ndipo malamulo anu ali m'kati mwamtima mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikufuna kuchita chifuniro chanu, Inu Mulungu wanga; lamulo lanu lili mu mtima mwanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kucita cikondwero canu kundikonda, Mulungu wanga; Ndipo malamulo anu ali m'kati mwamtima mwanga.