Psalms 40:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndalalika uthenga wabwino wa chipulumutso chanu pa msonkhano waukulu. Sindidatseke pakamwa, monga mukudziŵa, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndalalikira chilungamo mu msonkhano waukulu; onani, sindidzaletsa milomo yanga, mudziwa ndinu Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikulalikira uthenga wa chilungamo chanu mu msonkhano waukulu; sinditseka milomo yanga monga mukudziwa Inu Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndalalikira cilungamo mu msonkano waukuru; Onani, sindidzaletsa milomo yanga, Mudziwa ndinu Yehova.