Psalms 41:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukatero ndidzadziŵa kuti mumakondwera nane, chifukwa mdani wanga sadandipambane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, popeza mdani wanga sandiseka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikudziwa kuti mukukondwera nane, pakuti mdani wanga sandigonjetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, Popeza mdani wanga sandiseka.