Psalms 41:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwandichirikiza chifukwa cha kukhulupirika kwanga, mwandikhazika pamaso panu mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ine, mundigwirizize m'ungwiro wanga, ndipo mundiike pankhope panu kunthawi yamuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mu ungwiro wanga Inu mumandisunga ndi kundiyimika pamaso panu kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ine, mundigwirizize m'ungwiro wanga, Ndipo mundiike pankhope panu ku nthawi yamuyaya.