Psalms 41:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidati, “Inu Chauta, ndakuchimwirani, mundikomere mtima, muchiritse moyo wanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinati ine, Mundichitire chifundo, Yehova; Chiritsani mtima wanga; pakuti ndachimwira Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinati, “Inu Yehova, mundichitire chifundo; chiritseni pakuti ndakuchimwirani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinati ine, Mundicitire cifundo, Yehova: Ciritsani mtima wanga; pakuti ndacimwira Inu.