Psalms 41:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma adani anga ondifunira zoipa, amati, “Kodi munthu ameneyu adzafa liti, kuti aiŵalike?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adani anga andinenera choipa, ndi kuti, adzafa liti, ndi kutayika dzina lake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani anga mwankhwidzi amanena za ine kuti, “Kodi munthu ameneyu adzafa liti kuti ayiwalike?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adani anga andinenera coipa, ndi kuti, Adzafa liti, ndi kutayika dzina lace?