Psalms 41:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse odana nane amanong'onezana za ine, amayesa kuti zoipa zandigwera chifukwa cha kuipa kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse akudana nane andinong'onezerana; apangana chondiipsa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani anga onse amanongʼonezana pamodzi kulimbana nane, iwo amalingalira zoyipa kwambiri za ine, ponena kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse akudana nane andinong'onezerana; Apangana condiipsa ine.