Psalms 42:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe mbaŵala imakhumbira mtsinje wamadzi, ndimo m'mene mtima wanga umakhumbira Inu Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo. Chilangizo cha kwa ana a Kora. Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu, Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Ndakatulo ya ana a Kora. Monga mbawala ipuma wefuwefu kufunafuna mitsinje yamadzi, kotero moyo wanga upuma wefuwefu kufunafuna Inu Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; Motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu, Mulungu.