Psalms 42:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunyoza kwa adani anga kumandipweteka ngati bala lofa nalo la m'thupi mwanga, akamandifunsa nthaŵi zonse kuti, “Mulungu wako ali kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adani anga andinyoza ndi kundithyola mafupa anga; pakunena ndine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafupa anga ali ndi ululu wakufa nawo pamene adani anga akundinyoza, tsiku lonse akunena kuti, “Mulungu wako ali kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adani anga andinyoza ndi kundityola mafupa anga; Pakunena ndine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?