Psalms 42:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukumva ludzu lofuna Mulungu, Mulungu wamoyo. Kodi ndidzafika liti pamaso pa Mulungu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga uli ndi ludzu la kwa Mulungu, la kwa Mulungu wamoyo. Ndikadze liti kuoneka pamaso pa Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wanga uli ndi ludzu lofuna Mulungu, lofuna Mulungu wamoyo. Kodi ndipite liti kukakumana ndi Mulungu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga uli ndi ludzu la kwa Mulungu, la kwa Mulungu wamoyo: Ndikadze liti kuoneka pamaso pa Mulungu?