Psalms 42:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito yanga ndi kulira usana ndi usiku, osalaŵa chakudya chilichonse. Ndipo anthu akhala akunena kuti, “Mulungu wako ali kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Misozi yanga yakhala ngati chakudya changa, usana ndi usiku; pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Misozi yanga yakhala chakudya changa usana ndi usiku, pamene anthu akunena kwa ine tsiku lonse kuti, “Mulungu wako ali kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Misozi yanga yakhalangati cakudya canga, Usana ndi usiku; Pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?