Psalms 42:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndatayiratu mtima, nchifukwa chake ndikukumbukira Inu Mulungu, pamene ndili ku dziko la Yordani, ku Heremoni ndi ku phiri la Mizara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu wanga, moyo wanga udziweramira m'kati mwanga; chifukwa chake ndikumbukira Inu m'dziko la Yordani, ndi mu Aheremoni, m'kaphiri ka Mizara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wanga. Moyo wanga uli ndi chisoni mʼkati mwanga kotero ndidzakumbukira Inu kuchokera ku dziko la Yorodani, ku mitunda ya Herimoni kuchokera ku phiri la Mizara.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wanga, moyo wanga Udziweramira m'kati mwanga; Cifukwa cace ndikumbukila Inu m'dziko la Yordano, Ndi mu Ahermone, m'kaphiri ka Mizara.