Psalms 42:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Madzi akuya akuitanizana ndi madzi akuyanso, mathithi anu akulindima kochititsa mantha. Mafunde anu ang'onoang'ono ndi akuluakulu omwe andimiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, pa mkokomo wa matiti anu; mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzi akuya akuyitana madzi akuya mu mkokomo wa mathithi anu; mafunde anu onse obwera mwamphamvu andimiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, Pa mkokomo wa matiti anu: Mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.