Psalms 42:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Chauta amaonetsa chikondi chake chosasinthika tsiku ndi tsiku, Nchifukwa chake nthaŵi zonse ndimamuimbira nyimbo, ndi kumpemphera Mulungu wondipatsa moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma usana Yehova adzalamulira chifundo chake, ndipo usiku nyimbo yake idzakhala ndi ine. Inde pemphero la kwa Yehova wa moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma usana Yehova amalamulira chikondi chake, nthawi ya usiku nyimbo yake ili nane; pemphero kwa Mulungu wa moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma usana Yehova adzalamulira cifundo cace, Ndipo usiku Nyimbo yace idzakhala ndi ine. Inde pemphero la kwa Yehova wa moyowanga.