Psalms 43:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, onetsani kuti ine ndine wosalakwa, munditchinjirize pa mlandu wanga kwa anthu osasamala za Mulungu. Mundipulumutse kwa anthu onyenga ndi opanda chilungamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundiweruzire, Mulungu, ndipo mundinenere mlandu kwa anthu opanda chifundo. Mundilanditse kwa munthu wonyenga ndi wosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onetsani kusalakwa kwanga Inu Mulungu; ndipo mundinenere mlandu wanga kutsutsana ndi mtundu wosapembedza; mundilanditse mʼmanja mwa achinyengo ndi anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundiweruzire, Mulungu, ndipo mundinenere mlandu kwa anthu opanda cifundo: Mundilanditse kwa munthu wonyenga ndi wosalungama.