Psalms 43:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu Inu ndinu Mulungu wamphamvu amene ndimathaŵirako. Mwanditayiranji? Ndiziyenderanji ndilikulira chifukwa chondipsinja mdani wanga?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji? Ndimayenderanji woliralira chifukwa cha kundipsinja mdani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pajatu Inu Mulungu ndinu mphamvu zanga. Nʼchifukwa chiyani mwandikana ine? Nʼchifukwa chiyani ndiyenera kuyenda ndikulira, woponderezedwa ndi mdani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji? Ndimayenderanji woliralira cifukwa ca kundipsinja mdani?