Psalms 43:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidzapita ku guwa lansembe la Mulungu, kwa Mulungu amene amandipatsa chimwemwe chopambana. Ndipo ndidzakutamandani ndi pangwe, Inu Mulungu, Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti ndipite kufikira guwa la nsembe la Mulungu, kufikira Mulungu wa chimwemwe changa chenicheni, ndi kuti ndikuyamikeni ndi zeze, Mulungu, Mulungu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndidzapita ku guwa lansembe la Mulungu, kwa Mulungu, chimwemwe changa ndi chikondwerero changa. Ndidzakutamandani ndi zeze, Inu Mulungu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndipite kufikira guwa la nsembe la Mulungu, Kufikira Mulungu wa cimwemwe canga ceniceni: Ndi kuti ndikuyamikeni ndi zeze, Mulungu, Mulungu wanga.