Psalms 44:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwatisandutsa nkhosa zokaphedwa, mwatibalalitsa pakati pa mitundu ina ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwatipereka ngati nkhosa zoyenera kuzidya; ndipo mwatibalalitsa mwa amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munatipereka kuti tiwonongedwe monga nkhosa ndipo mwatibalalitsa pakati pa anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwatipereka ngati nkhosa zoyenera kuzidya; Ndipo mwatibalalitsa mwa amitundu.