Psalms 44:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwatisandutsa anthu onyozeka kwa anzathu oyandikana nafe, anthu otizungulira amatiseka ndi kutinyodola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutisandutsa chotonza kwa anzathu, ndi choseketsa ndi cholalatitsa iwo akutizinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachititsa kuti tikhale chochititsa manyazi kwa anthu a mitundu ina, chonyozeka ndi chothetsa nzeru kwa iwo amene atizungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutisandutsa cotonza kwa anzathu, Ndi coseketsa ndi colalatitsa iwo akutizinga.