Psalms 44:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwatisandutsa anthu oŵanyodola pakati pa anthu a mitundu ina, anthu omangosekedwa pakati pa anzathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutiika tikhale onyozeka mwa amitundu, ndi kuti anthu atipukusire mitu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachititsa kuti tikhale onyozeka pakati pa anthu a mitundu ina; anthu amapukusa mitu yawo akationa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutiika tikhale onyozeka mwa amitundu, Ndi kuti anthu atipukusire mitu.