Psalms 44:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lonse ndimangodziwona kuti ndine munthu wopandapake. Nkhope yanga yagwa chifukwa cha manyazi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lonse chimpepulo changa chikhala pamaso panga, ndipo manyazi a pankhope panga andikuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manyazi anga ali pamaso panga tsiku lonse ndipo nkhope yanga yaphimbidwa ndi manyazi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lonse cimpepulo canga cikhala pamaso panga, Ndipo manyazi a pankhope panga andikuta.