Psalms 44:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakumva mau a anthu onditonza ndi onditukwana, poona mdani wanga ndi munthu wolipsira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha mau a wotonza wochitira mwano; chifukwa cha mdani ndi wobwezera chilango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa cha mawu otonza a iwo amene amandinyoza ndi kundichita chipongwe, chifukwa cha mdani amene watsimikiza kubwezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca mau a wotonza wocitira mwano; Cifukwa ca mdani ndi wobwezera cilango,