Psalms 44:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikadaiŵala Mulungu wathu, kapena kugwadira mulungu wachilendo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tikadaiwala dzina la Mulungu wathu, ndi kutambasulira manja athu kwa mulungu wachilendo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tikanayiwala dzina la Mulungu wathu kapena kutambasulira manja athu kwa mulungu wachilendo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tikadaiwala dzina la Mulungu wathu, Ndi kutambasulira manja athu kwa mulungu wacilendo;