Psalms 44:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kodi Mulungu sakadazipeza zimenezi? Paja Iye amadziŵa zinsinsi zonse zamumtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu sakadasanthula ichi kodi? Pakuti adziwa zinsinsi za mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kodi Mulungu wathu sakanazidziwa zimenezi, pakuti Iye amadziwa zinsinsi zamumtima?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu sakadasanthula ici kodi? Pakuti adziwa zinsinsi za mtima.