Psalms 44:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma chifukwa cha Inu, adani akutipha tsiku lonse, pamaso pao tili ngati nkhosa zimene akukazipha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma, chifukwa cha Inu, tiphedwa tsiku lonse; tiyesedwa ngati nkhosa zakuzipha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe chifukwa cha Inu timakumana ndi imfa tsiku lonse, tili ngati nkhosa zoyenera kuti ziphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma, cifukwa ca Inu, tiphedwa tsiku lonse; Tiyesedwa ngati nkhosa zakuzipha.