Psalms 44:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mwatifulatira? Mwaiŵaliranji masautso athu ndi kupsinjidwa kwathu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mubisiranji nkhope yanu, ndi kuiwala kuzunzika ndi kupsinjika kwathu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu, ndi kuyiwala mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mubisiranji nkhope yanu, Ndi kuiwala kuzunzika ndi kupsinjika kwathu?