Psalms 44:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tagwa pansi m'fumbi, thupi lathu langoti thapsa pa dothi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti moyo wathu waweramira kufumbi, pamimba pathu pakangamira dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tatsitsidwa pansi mpaka pa fumbi; matupi athu amatirira pa dothi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti moyo wathu waweramira kupfumbi: Pamimba pathu pakangamira dziko lapansi.