Psalms 44:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzukani, mubwere kudzatithandiza. Tiwomboleni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukani, tithandizeni, tiomboleni mwa chifundo chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imirirani ndi kutithandiza, tiwomboleni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukani, tithandizeni, Tiomboleni mwa cifundo canu.