Psalms 44:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu ndinu Mfumu yanga ndi Mulungu wanga, amene mudampambanitsa Yakobe pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu ndinu mfumu yanga, Mulungu; lamulirani chipulumutso cha Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ndinu Mfumu yanga ndi Mulungu wanga amene mumalamulira chigonjetso cha Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu ndinu mfumu yanga, Mulungu: Lamulirani cipulumutso ca Yakobo.