Psalms 44:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi thandizo lanu tidakantha adani athu. Ndi mphamvu zanu tidapondereza ogalukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa Inu tidzakankhira pansi otsutsana nafe, m'dzina lanu tidzapondereza akutiukira ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kudzera kwa inu ife timabweza adani athu; kudzera mʼdzina lanu timapondereza otiwukirawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa Inu tidzakankhira pansi otsutsana nafe: M'dzina lanu tidzapondereza akutiukira ife.