Psalms 44:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu mwandilanditsa kwa adani athu, mwaŵachititsa manyazi amene amadana nafe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu munatipulumutsa kwa iwo akutsutsana nafe, ndipo akudana nafe, mudawachititsa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma Inu mumatigonjetsera adani athu, mumachititsa manyazi amene amadana nafe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu munatipulumutsa kwa iwo akutsutsana nafe, Ndipo akudana nafe, mudawacititsa manyazi.