Psalms 45:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mvera kuno, mkwati wamkaziwe, imva mau anga ndipo uŵaganizire bwino. Iŵala abale ako ndiponso nyumba ya bambo wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tamvera, mwana wamkaziwe, taona, tatchera khutu lako; uiwalenso mtundu wako ndi nyumba ya atate wako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamvera, iwe mwana wa mkazi ganizira ndipo tchera khutu; iwala anthu ako ndi nyumba ya abambo ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tamvera, mwana wamkaziwe, taona, tachera khutu lako; Uiwalenso mtundu wako ndi nyumba ya atate wako;