Psalms 45:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Tiro adzakukopa ndi mphatso, olemera kwambiri adzakunyengerera
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wamkazi wa Tiro adzafika nayo mphatso; achuma a mwa anthu adzapempha kudziwika nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa mkazi wa ku Turo adzabwera ndi mphatso, amuna a chuma adzafunafuna kukoma mtima kwako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wamkazi wa Turo adzafika nayo mphatso; Acuma a mwa anthu adzapempha kudziwika nanu.