Psalms 45:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi chuma chao chamitundumitundu. Mwana wamkazi wa mfumu ali m'chipinda mwake, wadzikongoletsa kwambiri, wavala zovala zoluka ndi thonje lagolide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwana wamkazi wa mfumu ngwa ulemerero wonse m'kati mwa nyumba, zovala zake nza malukidwe agolide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wokongola kwambiri ndi mwana wa mfumu ali mʼchipinda mwake, chovala chake ndi cholukidwa ndi thonje ndi golide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wamkazi wa mfumu ngwa ulemerero wonse m'kati mwa nyumba: Zobvala zace nza made agolidi.