Psalms 45:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akupita naye kwa mfumu atavala zovala zamaluŵa, pamodzi ndi anamwali anzake omperekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzamtsogolera kwa mfumu wovala zamawangamawanga, anamwali anzake omtsata adzafika nao kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atavala zovala zamaluwamaluwa akupita naye kwa mfumu; anamwali okhala naye akumutsatira ndipo abweretsedwa kwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzamtsogolera kwa mfumu wabvala zamawanga-mawanga: Anamwali anzace omtsata adzafika nao kwa inu.