Psalms 45:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzamveketsa mbiri ku mibadwo yonse, nchifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzawakumbutsa dzina lanu m'mibadwomibadwo; chifukwa chake mitundu ya anthu idzayamika Inu kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzabukitsa mbiri yako mʼmibado yonse; choncho mitundu yonse idzakutamanda ku nthawi za nthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzawakumbutsa dzina lanu m'mibadwo mibadwo: Cifukwa cace mitundu ya anthu idzayamika Inu ku nthawi za nthawi.