Psalms 45:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mivi yanu ndi yakuthwa, imalasa mitima ya adani. Mitundu ina ya anthu imagwa pansi pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mivi yanu njakuthwa; mitundu ya anthu igwa pansi pa inu; iwalasa mumtima adani a mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mivi yanu yakuthwa ilase mitima ya adani a mfumu, mitundu ya anthu igwe pansi pa mapazi anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mibvi yanu njakuthwa; Mitundu ya anthu igwa pansi pa Inu: Iwalasa mumtima adani a mfumu.