Psalms 45:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu, ndi wamuyaya, mumaweruza molungama mu ufumu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mpando wachifumu wanu, Mulungu, ukhala nthawi zonse zomka muyaya. Ndodo yachifumu ya ufumu wanu ndiyo ndodo yolunjika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu, udzakhala ku nthawi za nthawi; ndodo yaufumu yachilungamo idzakhala ndodo yaufumu ya ufumu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpando wacifumu wanu, Mulungu, ukhala nthawi zonse zamkamuyaya: Ndodo yacifumu ya ufumu wanu ndiyo ndodo yolunjika.