Psalms 45:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ana aakazi a mafumu ali m'gulu la mbumba zanu zolemekezeka. Ku dzanja lanu lamanja kwaima mfumukazi, yovala zovala za golide wa ku Ofiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa omveka anu muli ana akazi a mafumu; ku dzanja lanu lamanja aima mkazi wa mfumu wovala golide wa ku Ofiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aakazi a mafumu ali pakati pa akazi anu olemekezeka; ku dzanja lanu lamanja kuli mkwatibwi waufumu ali mu golide wa ku Ofiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa omveka anu muli ana akazi amafumu: Ku dzanja lamanja lanu aima mkazi wa mfumu wobvala golidi wa ku Ofiri.