Psalms 46:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Khalani chete, ndipo mudziŵe kuti ndine Mulungu. Mitundu ya anthu imanditamanda, a m'dziko lapansi amandiyamika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khalani chete, ndipo dziwani kuti Ine ndine Mulungu, Ndidzabuka mwa amitundu, ndidzabuka pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuti, “Khala chete, ndipo dziwa kuti ndine Mulungu; ndidzakwezedwa pakati pa mitundu ya anthu; ine ndidzakwezedwa mʼdziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khalani cete, ndipo dziwani kuti Ine ndine Mulungu: Ndidzabuka mwa amitundu, Ndidzabuka pa dziko lapansi.