Psalms 46:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake sitidzaopa ngakhale dziko lapansi lisinthike, ngakhale mapiri agwe pakati pa nyanja zozama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake sitidzachita mantha, lingakhale lisandulika dziko lapansi, angakhale mapiri asunthika, nakhala m'kati mwa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake sitidzaopa ngakhale dziko lapansi lisunthike, ngakhale mapiri agwe pakati pa nyanja,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace sitidzacita mantha, lingakhale lisandulika dziko lapansi, Angakhale mapiri asunthika, nakhala m'kati mwa nyanja;