Psalms 46:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngakhale nyanja zikokome ndi kututuma. Ngakhale mapiri anjenjemere ndi kulindima kwa nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana madzi ake akokoma, nachita thovu, nagwedezeka mapiri ndi kudzala kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale madzi ake atakokoma ndi kuchita thovu, ngakhale mapiri agwedezeke ndi kukokoma kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana madzi ace akokoma, nacita thobvu, Nagwedezeka mapiri ndi kudzala kwace.